Contact us on Facebook

Zongoikidwa Kumene

Updates : Songout to Jehovah Joyfully Added On Tue, 23 Apr 2024 (17:05)
New
Updates : Nzeru Zopezeka m'Mabuku a Uthenga Wabwino Added On Tue, 23 Apr 2024 (16:50)
New
Updates : Kodi zinangochitika zokha? Added On Tue, 23 Apr 2024 (16:13)
New
Updates : 2024 - Kuphunzira Malemba tsiku ndi tsiku Added On Mon, 22 Apr 2024 (17:18)
New
Updates : Lalikira Mawu - Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2024 Added On Mon, 22 Apr 2024 (16:01)
New
[Onani Zinanso...]

Kodi a Mboni za Yehova Mumawadziwa?



Ndife anthu ochokera m’mitundu, zikhalidwe ndiponso zinenero zosiyanasiyana, koma ndife ogwirizana kwambiri chifukwa cholinga chathu n’chimodzi.

Cholinga chathu chachikulu n’kulemekeza Yehova,Mulungu wotchulidwam’Baibulo ndiponso Mlengi wa zinthu zonse. Timayesetsa kutsanzira Yesu Khristu ndipo timanyadira kutchedwa Akhristu. Nthawi zonse aliyense wa ife amathera nthawi yake pothandiza ena kuphunzira Baibulo ndiponso za Ufumu wa Mulungu.

Timatchedwa kuti Mboni za Yehova chifukwa choti timachitira umboni, kapena kuti kulalikira za Yehova Mulungu ndi Ufumu wake.

Ngati mungakonde, mukhonza kupempha kuti a Mboni adzakuyendereni kuti adzaphunzire nanu Baibulo
Sign in here